\v 8 Bonse ni bakaswili na lupanga ndipo nioziba nkhondo. Muntu aliyense ali na lupanga yake m'msana mwake, okonzekela ndi zoyofiya za usiku. \v 9 Mfumu Solomo anzipangira yekha mpando wamatabwa wochokera ku Lebanoni.