\c 6 \v 1 Wokondedwa wako wapita kuti, iwe wokongola kwambiri mwa akazi onse? Wokondedwa wanu wapita kuti, kuti tikamuyese limodzi nanu? Mkazi akuyankhula yekha