\v 3 "Navula mukanjo wanga; niyenela futi kuuvala? Nasuka mendo yanga; kodi niyafipise?" \v 4 Okondewa wanga ana genesa kwanja kwake pa nyumba ya chiseko, ndipo mutima wanga una khudziwa chifukwa cha eve.