\v 5 Ndidadzuka kuti ndimutsegulire wokondedwa wanga; manja anga anali kutulutsa mure, zala zanga ndi mule wonyowa, pachipata cha chitseko.