\v 15 Nvela ,ndiwe okongola, okondewa wanga; vela, ndiwe okongola; menso wako ali ngati nkunda.