\c 8 \v 1 Nikulakalaka sembe unakhala ngati mubale wanga, wamene ananyoka mabele ba mai banga. Ndipo nthawi zonse nikakukumana iwe panja, niga kufyofyonte, ndipo palibe wamene aganinyoza.