\v 10 Okondewa wanga anani kambisa kuti, uka, okodewa wanga; okongola wanga, tiye, \v 11 Ona, mpepo yapita; mvula yapita, yayenda.