\v 8 Ngati suziba ,okongola kwambili pakhati pali bakazi bonse, kokani njila ya nkosa zanga, ndipo dyeselani bana banu ba mbuzi pafupi na mahema yamu busa.