\v 16 Wokondewa wanga ni wanga, ndipo ine ndine wake; adyela pakati pa maluba mwachisangalalo \v 17 Yenda, wokondewa wanga, mphepo yam'tandakucha isanabwele na chiuviliuvili chisana yende . Chokani; khala ngati mphoyo, kapena nswala pa mapiri olimba.