\v 4 Ndiwe okongola kwati Tiriza, okondewa wanga, okongola ngati Yelusalemu, wochititsa- mantha ngati gulu ya khondo yokhala na mbendera yake.