\c 5 \v 1 Nabwela mu munda mwanga, mlongo wanga, muwatibwi wanga; Nasonkanisa mure wanga na zonunkirisa zanga. Nadya chisa changa cha uchi na uchi wanga. Namwa vinyu wanga pamodzi na mukaka wanga.