\v 8 bwela naine kuchoka mu Lebanoni, mukwatibwi wanga. Bwelani naine ku choka ku Lebanoni; choka pa mwamba pa Amana, pamwamba pa Senili na Hermoni, mumapanga ya nkalamu, kuchoka muma pili ya mapanga ya kaingu.