\v 12 Tiye tiuke kuseniseni tiyende ku minda ya mphesa; tiye tikaone ngati mipesa yaphuka, kaya maluba yake yaseguka, kapena ngati makangaza yali na maluba. Kwamenekuja niza kupasa chikondi changa.