\v 5 Mutu wako uli pa iwe kwati Karimeli; sisi yaku mutu kwako ni lofiilila. Mfumuyo imagwidwa ukapolo ni zikakamizo zake. \v 6 Okongola, ndiwe okongola bwanji, okondewa wanga!