\v 2 Muhombo wako uli kwati mubale mozunguka; lekani isakasobe vinyu vosankaniza. Mimba yako ili kwati cho umba cha tiligu chozunguluka na maluba.