\v 10 Okondewa wanga ni owala na maonekedwe yabwino, opambana pakati pa zikwi khumi. \v 11 Mutu wake ni golide woyengeka bwino; sisi yake ni yopobana koma yakuda ngati kwangwala.