\v 6 Nina segula chiseko cha okondewa wanga, koma okondewa wanga ana pidamuka naku yenda. Mutima wanga unagwa pamene anakamba. Nina mufunafuna, koma sinina mupeza; Nina muitana, koma sanani yanke.