\v 3 Milomo yanu ili kwati ulusi wofila kwambili; mukamwa mwako ndiwe okongola. Masaya yako yali kwati makangaza ya makangaza kuseli kwa chophimba chako.