\v 12 Maluwa yaonekela paziko ya pansi; ntawi yodulia na kuimba kwa nyoni yafika, ndipo phokoso ya nkunda ya mveka mu ziko yatu. \v 13 Mutengo wa mukuyu yapya nkuyu wake yobiliwila, ndipo mipesa yachita maluba; zipeleka fungo yake. Nyamuka, okodewa wanga, okongola wanga, tiye tiziyenda.