\c 2 \v 1 Ine ndine duwa ya ku Sharoni, kakombo wa muzigwa. \v 2 Ngati kakombo pakati pa minga, chamene icho chikondi changa pakati pa asikana.