Fri Sep 22 2017 09:25:05 GMT+0200 (Central Africa Time)

This commit is contained in:
tsDesktop 2017-09-22 09:25:06 +02:00
parent 23c5e25f20
commit f9c5b5e30a
2 changed files with 2 additions and 2 deletions

View File

@ -1 +1 @@
\v 10 Wokondewa wanga ananikabisa kuti, uka, okodewa wanga; wokongola wanga, tiye, \v 11 Ona, mpepo yapita; mvula yapita, natha.
\v 10 Wokondewa wanga ananikabisa kuti, uka, okodewa wanga; wokongola wanga, tiye, \v 11 Ona, mpepo yapita; mvula yapita, yayenda.

View File

@ -1 +1 @@
\v 12 Maluwawo awonekera padziko lapansi; nthawi yodulira ndi kuimba kwa mbalame yafika, ndipo phokoso la nkhunda lamveka m'dziko lathu. \v 13 Mtengo wa mkuyu upsa nkhuyu zake zobiriwira, ndipo mipesa yachita maluwa; amapereka fungo lawo. Nyamuka, bwenzi langa, wokongola wangawe, tiye tizipita.
\v 12 Maluwa yaonekera padziko lapansi; nthawi yodulira ndi kuimba kwa mbalame yafika, ndipo phokoso la nkhunda lamveka m'dziko lathu. \v 13 Mtengo wa mkuyu upsa nkhuyu zake zobiriwira, ndipo mipesa yachita maluwa; amapereka fungo lawo. Nyamuka, bwenzi langa, wokongola wangawe, tiye tizipita.