diff --git a/04/10.txt b/04/10.txt index 95507a0..6b26e68 100644 --- a/04/10.txt +++ b/04/10.txt @@ -1 +1 @@ -\v 10 Ni wokongola bwanji chikondi chako, mlongo wanga, mkwatibwi wanga! Chikondi chako chiposa vinyo motani, ndi fungo labwino la zonunkhira zako kuposa zonunkhiritsa zilizonse. \v 11 Milomo yako, mkwatibwi, ikukha uchi; uchi ndi mkaka zili pansi pa lilime lako; kununkhira kwa zovala zako ndikununkhira kwa Lebano. \ No newline at end of file +\v 10 Nichabwino bwanji chikondi chako, mulongo wanga, mukwatibwi wanga! Nanga chikondi chako chiposa vinyo motani, ndi fungo labwino la zonunkhira zako kuposa zonunkhiritsa zilizonse. \v 11 Milomo yako, mkwatibwi, ikukha uchi; uchi ndi mkaka zili pansi pa lilime lako; kununkhira kwa zovala zako ndikununkhira kwa Lebano. \ No newline at end of file