From e43862ed735bc885dbeecdf15f7e7476270a38ff Mon Sep 17 00:00:00 2001 From: tsDesktop Date: Thu, 7 Oct 2021 13:14:08 +0200 Subject: [PATCH] Thu Oct 07 2021 13:14:08 GMT+0200 (Central Africa Time) --- 01/07.txt | 1 + 01/08.txt | 1 + 01/09.txt | 1 + 01/12.txt | 1 + manifest.json | 6 +++++- 5 files changed, 9 insertions(+), 1 deletion(-) create mode 100644 01/07.txt create mode 100644 01/08.txt create mode 100644 01/09.txt create mode 100644 01/12.txt diff --git a/01/07.txt b/01/07.txt new file mode 100644 index 0000000..a770ff8 --- /dev/null +++ b/01/07.txt @@ -0,0 +1 @@ +\v 7 Ndiwuze, iwe amene mtima wanga umakonda, umadyetsera ziweto zako kuti? Umapumitsa kuti ziweto zako nthawi yamasana? Ndisandukire bwanji munthu wakungoyendayenda ndi gulu la abale ako? \ No newline at end of file diff --git a/01/08.txt b/01/08.txt new file mode 100644 index 0000000..2f94c6e --- /dev/null +++ b/01/08.txt @@ -0,0 +1 @@ +\v 8 Mwamuna akuyankhula ndi mkazi Ngati simukudziwa, wokongola kwambiri pakati pa akazi onse, tsatirani njira za nkhosa zanga, ndipo odyetserani ana anu a mbuzi pafupi ndi mahema a abusa. \ No newline at end of file diff --git a/01/09.txt b/01/09.txt new file mode 100644 index 0000000..a7b25ea --- /dev/null +++ b/01/09.txt @@ -0,0 +1 @@ +\v 9 Wokondedwa wanga, ndakufanizitsa ndi mwana wamkazi wa mahatchi a Farao. \v 10 Masaya ako ndi abwino ndi zokongoletsera, khosi lako ndi zokongoletsa za zingwe. \v 11 Tikupangira zokongoletsera zagolide ndi zomangira zasiliva. Mkazi akuyankhula yekha \ No newline at end of file diff --git a/01/12.txt b/01/12.txt new file mode 100644 index 0000000..50c0e26 --- /dev/null +++ b/01/12.txt @@ -0,0 +1 @@ +\v 12 Mfumu ili chigonere pabedi pake, nade wanga anali kutulutsa kununkhira kwake. \v 13 Wokondedwa wanga ali ngati thumba la mule limene limagona pakati pa mabere anga usiku wonse. \v 14 Wokondedwa wanga ali kwa ine ngati tsango la maluwa a heni m'minda yamphesa ya En-Gedi. \ No newline at end of file diff --git a/manifest.json b/manifest.json index f289489..d7976bf 100644 --- a/manifest.json +++ b/manifest.json @@ -39,6 +39,10 @@ "front-title", "01-title", "01-01", - "01-05" + "01-05", + "01-07", + "01-08", + "01-09", + "01-12" ] } \ No newline at end of file