Thu Oct 07 2021 14:00:23 GMT+0200 (Central Africa Time)
This commit is contained in:
parent
0d3496d3c8
commit
c98ddc5ca6
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
Mkazi wolankhula ndi akazi amzinda \v 10 Wokondedwa wanga ndi wowala ndi wofiira, wopambana pakati pa zikwi khumi. \v 11 Mutu wake ndi golide woyengeka bwino; tsitsi lake ndi lopotana komanso lakuda ngati khwangwala.
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 12 Maso ake akunga nkhunda pambali pa mitsinje yamadzi; osambitsidwa ndi mkaka, atakwera ngati miyala yamtengo wapatali.
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 13 Masaya ake ali ngati mabedi a zonunkhira, zonunkhira bwino. Milomo yake ili ngati maluwa, akuchucha mure.
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
Manja ake ali ndi golidi wozunguliridwa ndi miyala yamtengo wapatali. Mimba yake ndi minyanga ya njovu yokutidwa ndi miyala ya safiro.
|
|
@ -83,6 +83,9 @@
|
|||
"05-06",
|
||||
"05-07",
|
||||
"05-08",
|
||||
"05-09"
|
||||
"05-09",
|
||||
"05-10",
|
||||
"05-12",
|
||||
"05-13"
|
||||
]
|
||||
}
|
Loading…
Reference in New Issue