From abe5f4f25292cf420eddc9835c0cde05abcafcce Mon Sep 17 00:00:00 2001 From: tsDesktop Date: Thu, 7 Oct 2021 13:48:20 +0200 Subject: [PATCH] Thu Oct 07 2021 13:48:20 GMT+0200 (Central Africa Time) --- 03/03.txt | 1 + 03/05.txt | 1 + 03/06.txt | 1 + 03/08.txt | 1 + manifest.json | 6 +++++- 5 files changed, 9 insertions(+), 1 deletion(-) create mode 100644 03/03.txt create mode 100644 03/05.txt create mode 100644 03/06.txt create mode 100644 03/08.txt diff --git a/03/03.txt b/03/03.txt new file mode 100644 index 0000000..8e5065d --- /dev/null +++ b/03/03.txt @@ -0,0 +1 @@ +\v 3 Alonda anandipeza pamene anali kuzungulira mzindawo. Ndinawafunsa kuti, "Kodi mwaona amene moyo wanga umam'konda?" \v 4 Panangopita kanthawi pang'ono nditadutsa kumene ndipo ndinamupeza amene moyo wanga umamukonda. Ndinamugwira ndipo sindimulola apite kufikira nditamutengera m mother'snyumba ya amayi anga, m thechipinda chogona cha amene anandipatsa pakati. \ No newline at end of file diff --git a/03/05.txt b/03/05.txt new file mode 100644 index 0000000..eaffa16 --- /dev/null +++ b/03/05.txt @@ -0,0 +1 @@ +\v 5 Mkazi amene akulankhula ndi akazi ena ndikufuna ndikulumbire, ana akazi inu a ku Yerusalemu, ndi mphoyo ndi nswala za kuthengo, kuti simudzadzutsa kapena kudzutsa chikondi kufikira atakondwera. \ No newline at end of file diff --git a/03/06.txt b/03/06.txt new file mode 100644 index 0000000..3a130f9 --- /dev/null +++ b/03/06.txt @@ -0,0 +1 @@ +\v 6 Mkazi akudziyankhulila yekha 6Ndi ciani cikukwera kucokera kucipululu ngati utsi, wakudzola ndi mure, ndi lubani, ndi ufa wathunthu wogulitsidwa ndi amalonda? \v 7 Taonani, ndi kama wa Solomo; Ankhondo makumi asanu ndi limodzi akuzungulira, Amuna amphamvu a mu Israeli. \ No newline at end of file diff --git a/03/08.txt b/03/08.txt new file mode 100644 index 0000000..2c3ef27 --- /dev/null +++ b/03/08.txt @@ -0,0 +1 @@ +\v 8 Onsewo ndi aluso ndi lupanga ndipo ngodziwa nkhondo. Munthu aliyense ali ndi lupanga lake m'chiuno mwake, atakonzeka ndi zoopsa za usiku. \v 9 Mfumu Solomo idadzipangira nokha mpando wamatabwa wochokera ku Lebanoni. \ No newline at end of file diff --git a/manifest.json b/manifest.json index 0c06f58..610b6a8 100644 --- a/manifest.json +++ b/manifest.json @@ -58,6 +58,10 @@ "02-15", "02-16", "03-title", - "03-01" + "03-01", + "03-03", + "03-05", + "03-06", + "03-08" ] } \ No newline at end of file