Thu Oct 07 2021 13:52:21 GMT+0200 (Central Africa Time)
This commit is contained in:
parent
77b1cc5c36
commit
7abc63d7e2
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 4 Khosi lako lili ngati nsanja ya Davide yomangidwa m'mizere yamiyala, yokhala ndi zishango chikwi pa iyo, zishango zonse za ankhondo. \v 5 Mabere ako awiri ali ngati ana awiri, amapasa a insa, akudya msipu pakati pa maluwa.
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 6 Mpaka mbandakucha ndi mithunzi ithawe, ndipita kuphiri la mure ndi kuphiri la lubani. \v 7 Ndiwe wokongola m'njira zonse, wokondedwa wanga ndipo palibe chilema mwa iwe.
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 8 Tiye kuno ku Lebanoni, iwe mkwatibwi wanga. Bwerani nane kuchokera ku Lebanoni; amachokera pamwamba pa Amana, pamwamba pa Seniri ndi Hermoni, m'mapanga a mikango, m'mapanga a akambuku.
|
|
@ -0,0 +1 @@
|
|||
\v 9 Waba mtima wanga, mlongo wanga, mkwatibwi wanga; mwaba mtima wanga, pondiyang'ana kamodzi, ndi mwala umodzi wa mkanda wanu.
|
|
@ -67,6 +67,10 @@
|
|||
"04-title",
|
||||
"04-01",
|
||||
"04-02",
|
||||
"04-03"
|
||||
"04-03",
|
||||
"04-04",
|
||||
"04-06",
|
||||
"04-08",
|
||||
"04-09"
|
||||
]
|
||||
}
|
Loading…
Reference in New Issue