diff --git a/02/16.txt b/02/16.txt index 0ac9e99..a794d84 100644 --- a/02/16.txt +++ b/02/16.txt @@ -1 +1 @@ -\v 16 Wokondewa wanga ni wanga, ndipo ine ndine wake; adyela pakati pa maluba mwachisangala \v 17 Pita, wokondedwa wanga, mphepo yam'bandakucha isanagwe ndi mithunzi isanachoke. Chokani; khala ngati mphoyo, kapena nswala pa mapiri olimba. \ No newline at end of file +\v 16 Wokondewa wanga ni wanga, ndipo ine ndine wake; adyela pakati pa maluba mwachisangalalo \v 17 Yenda, wokondewa wanga, mphepo yam'tandakucha isanagwe ndi mithunzi isanachoke. Chokani; khala ngati mphoyo, kapena nswala pa mapiri olimba. \ No newline at end of file