Thu Sep 21 2017 09:35:19 GMT+0200 (Central Africa Time)

This commit is contained in:
tsDesktop 2017-09-21 09:35:20 +02:00
parent b249d9345f
commit 564953011d
1 changed files with 1 additions and 1 deletions

View File

@ -1 +1 @@
\v 3 Mkazi wolankhula yekha Ngati mtengo wa apurikoti pakati pa mitengo ya m'nkhalango, momwemonso wokondedwa wanga pakati pa anyamata. Ndimakhala pansi pamthunzi wake mosangalala kwambiri, ndipo zipatso zake ndi zotsekemera pakumva kwanga. \v 4 Anandibweretsa kunyumba ya vinyo, ndipo chikwangwani chake pa ine chinali chikondi. Mkazi amalankhula ndi mwamunayo
\v 3 Mkazi azikambisa yekha Ngati mtengo wa apurikoti pakati pa mitengo ya m'nkhalango, momwemonso wokondedwa wanga pakati pa anyamata. Ndimakhala pansi pamthunzi wake mosangalala kwambiri, ndipo zipatso zake ndi zotsekemera pakumva kwanga. \v 4 Anandibweretsa kunyumba ya vinyo, ndipo chikwangwani chake pa ine chinali chikondi. Mkazi amalankhula ndi mwamunayo