Thu Oct 07 2021 14:08:22 GMT+0200 (Central Africa Time)

This commit is contained in:
tsDesktop 2021-10-07 14:08:23 +02:00
parent 039e42369b
commit 3d8c77ebcc
6 changed files with 10 additions and 1 deletions

1
07/01.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\c 7 \v 1 Mapazi ako awoneka okongola bwanji mu nsapato zako, mwana wamkazi wa kalonga! Ntchafu zako ndizo zopindika bwino, zokongola kwambiri, ntchito ya manja a mmisiri waluso.

1
07/02.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 2 Mchombo wako uli ngati mbale yozungulira; isasowe vinyo wosanganiza. Mimba yako ili ngati chitunda cha tirigu chozunguliridwa ndi maluwa.

1
07/03.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 3 Mabere ako awiri ali ngati ana awiri amapasa a insa. \v 4 Khosi lako lili ngati nsanja yaminyanga ya njovu; maso ako ali ngati mayiwe a ku Hesiboni, pafupi ndi chipata cha Bath Rabbim. Mphuno yako ili ngati nsanja ya ku Lebanoni yomwe imayang'ana ku Damasiko.

1
07/05.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 5 Mutu wako uli pa iwe ngati Karimeli; tsitsi lakumutu kwako ndi lofiirira. Mfumuyo imagwidwa ukapolo ndi zikakamizo zake. \v 6 Wokongola, ndiwe wokongola bwanji, wokondedwa wanga!

1
07/07.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 7 Kutalika kwako kuli ngati mtengo wa kanjedza, ndipo mabere ako ali ngati masango a zipatso. \v 8 Ndinati, "Ndikufuna kukwera mtengo wa mgwalangwawo; ndigwira nthambi zake." Mabere ako akhale ngati zipatso za mphesa, Ndipo fungo la m'mphuno mwako likhale ngati apurikoti.

View File

@ -100,6 +100,10 @@
"06-10", "06-10",
"06-11", "06-11",
"06-13", "06-13",
"07-title" "07-title",
"07-01",
"07-02",
"07-03",
"07-05"
] ]
} }