diff --git a/02/08.txt b/02/08.txt index ebf81bb..a5aa0aa 100644 --- a/02/08.txt +++ b/02/08.txt @@ -1 +1 @@ -\v 8 Pali phokoso kwa wokondedwa wanga! Mverani, apa abwera, akudumpha pamapiri, nakujumpha pamapiri. \v 9 Wokondewa wanga ali ngati mbawala kapena mwana wa mphoyo; onani, wayimirira kuseri kwa khoma lathu, akuyang'anisisa pazenera, asuzumira pazenera. \ No newline at end of file +\v 8 Pali phokoso pali okondewa wanga! Mvelani, apa abwela, akudumpha pamapiri, nakujumpha pamapiri. \v 9 Wokondewa wanga ali ngati mbawala kapena mwana wa mphoyo; onani, wayimirira kuseri kwa khoma lathu, akuyang'anisisa pazenera, asuzumira pazenera. \ No newline at end of file