Fri Sep 22 2017 17:45:26 GMT+0200 (Central Africa Time)

This commit is contained in:
tsDesktop 2017-09-22 17:45:27 +02:00
parent 1842c97b75
commit 35cb27faba
1 changed files with 1 additions and 1 deletions

View File

@ -1 +1 @@
\c 3 \v 1 Usiku nili pabedi yanga ninalakalaka amene moyo wanga umkonda; Ndinamfunafuna, koma sindinamupeze. \v 2 Ndinati kwa ine, "Ndidzuka ndi kupyola pakati pa mzinda, m'misewu ndi m'mabwalo; ndidzafufuza amene moyo wanga umkonda." Ndinamfunafuna koma sindinamupeze.
\c 3 \v 1 Usiku nili pabedi yanga nalakalaka amene moyo wanga umkonda; Ndinamfunafuna, koma sindinamupeze. \v 2 Ndinati kwa ine, "Ndidzuka ndi kupyola pakati pa mzinda, m'misewu ndi m'mabwalo; ndidzafufuza amene moyo wanga umkonda." Ndinamfunafuna koma sindinamupeze.