Tue Sep 26 2017 20:19:19 GMT+0200 (Central Africa Time)

This commit is contained in:
tsDesktop 2017-09-26 20:19:20 +02:00
parent 0ec3bf9b77
commit 1678f74639
1 changed files with 1 additions and 1 deletions

View File

@ -1 +1 @@
\v 12 Mlongo wanga, mkwatibwi wanga ni munda ovaliwa, munda ovaliwa, kasupe ovaliwa. \v 13 Misambo zanu na munda wa makangaza na zipaso zabwino kwambiri, ni zipaso za henna ni nado, \v 14 nado ndi safironi, kalamusi ndi sinamoni wokhala ndi mitundu yonse ya zonunkhiritsa, mure ndi aloye ndi zonunkhira zabwino koposa.
\v 12 Mlongo wanga, muwatibwi wanga ni munda ovaliwa, munda ovaliwa, kasupe ovaliwa. \v 13 Misambo zanu na munda wa makangaza na zipaso zabwino kwambiri, ni zipaso za henna ni nado, \v 14 nado na safironi, kalamusi na sinamoni wokhala ndi mitundu yonse ya zonunkhiritsa, mure ndi aloye ndi zonunkhira zabwino koposa.