Fri Sep 22 2017 19:03:26 GMT+0200 (Central Africa Time)

This commit is contained in:
tsDesktop 2017-09-22 19:03:30 +02:00
parent 08ac0c39bb
commit 15d7af599e
1 changed files with 1 additions and 1 deletions

View File

@ -1 +1 @@
\v 10 Nsanamira zake zinali za siliva; kubuyo kwake kwenze kwagolide, na mpando wa nyula zofiirira. Mkati mwake munakongoletsewa na chikondi na bana bakazi ba ku Yerusalemu. \v 11 Yedani bana ba kazi baku Ziyoni, ndipo yang'anani Mfumu Solomo, atanyamula chisoti chachifumu chimene amayi ake anamveka pa tsiku laukwati wake, pa tsikulo. za chisangalalo cha mtima wake.
\v 10 Nsanamira zake zinali za siliva; kubuyo kwake kwenze kwagolide, na mpando wa nyula zofiirira. Mkati mwake munakongoletsewa na chikondi na bana bakazi ba ku Yerusalemu. \v 11 Yedani bana ba kazi baku Ziyoni, ndipo yang'anani Mfumu Solomo, letani chisote chachifumu chimene amayi bake banamvelika pa tsiku laukwati wake, pa tsikulo. za chisangalalo cha mtima wake.