From 039e42369b56b3cece64a6d90be26da8f26a0f6e Mon Sep 17 00:00:00 2001 From: tsDesktop Date: Thu, 7 Oct 2021 14:06:23 +0200 Subject: [PATCH] Thu Oct 07 2021 14:06:22 GMT+0200 (Central Africa Time) --- 06/08.txt | 2 +- 06/10.txt | 1 + 06/11.txt | 1 + 06/13.txt | 1 + 07/title.txt | 1 + manifest.json | 7 ++++++- 6 files changed, 11 insertions(+), 2 deletions(-) create mode 100644 06/10.txt create mode 100644 06/11.txt create mode 100644 06/13.txt create mode 100644 07/title.txt diff --git a/06/08.txt b/06/08.txt index a208b29..34ab3bd 100644 --- a/06/08.txt +++ b/06/08.txt @@ -1 +1 @@ -\v 8 \v 9 Pali mafumukazi makumi asanu ndi limodzi, adzakazi makumi asanu ndi atatu, ndi atsikana osawerengeka. Nkhunda yanga, yosadetsedwa, ndiyo yokhayo; ndiye mwana wamkazi m'modzi yekha wa amake; ndiye wokondedwa kwambiri mwa mkazi amene adamubala. Atsikana anamuwona ndipo anamutcha wodala; mfumukazi ndi adzakazi adamuwonanso, ndipo adamtamanda: Zomwe mfumukazi ndi adzakazi adanena \ No newline at end of file +\v 8 Pali mafumukazi makumi asanu ndi limodzi, adzakazi makumi asanu ndi atatu, ndi atsikana osawerengeka. \v 9 Nkhunda yanga, yosadetsedwa, ndiyo yokhayo; ndiye mwana wamkazi m'modzi yekha wa amake; ndiye wokondedwa kwambiri mwa mkazi amene adamubala. Atsikana anamuwona ndipo anamutcha wodala; mfumukazi ndi adzakazi adamuwonanso, ndipo adamtamanda: Zomwe mfumukazi ndi adzakazi adanena \ No newline at end of file diff --git a/06/10.txt b/06/10.txt new file mode 100644 index 0000000..37f7b9f --- /dev/null +++ b/06/10.txt @@ -0,0 +1 @@ +\v 10 "Ndani uyu amene akuwoneka ngati mbandakucha, wokongola ngati mwezi, wowala ngati dzuwa, wowopsa ngati gulu lankhondo lokhala ndi mbendera zake?" Mwamunayo amalankhula yekha \ No newline at end of file diff --git a/06/11.txt b/06/11.txt new file mode 100644 index 0000000..5250655 --- /dev/null +++ b/06/11.txt @@ -0,0 +1 @@ +\v 11 Ndidatsikira kumunda wamitengo kuti ndikawone kakulidwe kamene kali m'chigwacho, kuti ndikawone ngati mipesa idaphukira, kapena ngati makangaza ali pachimake. \v 12 Ndinali wokondwa kwambiri kuti ndimamva kuti ndinkakwera galeta la kalonga abwenzi akuyankhula ndi mayiyo \ No newline at end of file diff --git a/06/13.txt b/06/13.txt new file mode 100644 index 0000000..397a804 --- /dev/null +++ b/06/13.txt @@ -0,0 +1 @@ +\v 13 Bwerera, bwerera m'mbuyo, Msulami iwe! Bwerera, tibwerere kuti tikakuyang'ane! Mkazi amene akuyankhula ndi anzakewo N'chifukwa chiyani mwaona Msulami, ngati kuti mukuvina gombe la Mahanaimu? \ No newline at end of file diff --git a/07/title.txt b/07/title.txt new file mode 100644 index 0000000..a692fe4 --- /dev/null +++ b/07/title.txt @@ -0,0 +1 @@ +Mutu 7 \ No newline at end of file diff --git a/manifest.json b/manifest.json index b97e58d..56d62b8 100644 --- a/manifest.json +++ b/manifest.json @@ -95,6 +95,11 @@ "06-02", "06-04", "06-05", - "06-06" + "06-06", + "06-08", + "06-10", + "06-11", + "06-13", + "07-title" ] } \ No newline at end of file