nya-x-nyanja_sng_text_reg/04/01.txt

1 line
189 B
Plaintext
Raw Normal View History

\c 4 \v 1 Ha, ndiwe wokongola, okondewa wanga; ndiwe wokongola. Menso yako yali ngati nkhunda kuseri kwa chovinikila chako. sisi yako ili ngati gulu ya mbuzi yochokira ku phiri ya Giliyadi.