2017-10-01 21:54:53 +00:00
|
|
|
\v 7 Kutalimpa kwako kuli kwati mutengo wa kanjeza, ndipo mabele yako yali kwati gulu ya ba paso. \v 8 Nina kamba kuti, "Nifuna kukwela mutengo wa kanjeza; nizagwila misabo zake." Mabele yako ya nkale kwati zipatso za mphesa, Ndipo fungoyla mpuno yako inkale kwati apulikoti.
|