nya-x-nyanja_sng_text_reg/01/12.txt

1 line
255 B
Plaintext
Raw Normal View History

\v 12 Mfumu ili gone pabedi pake, nade wanga anali kuchosa kununkila kwake. \v 13 Wokondewa wanga alimonga tumba ya mule yamene imagona pakati pa mabere yanga. \v 14 Wokondewa wanga ali ngati kuli ine tsango la maluwa a heni m'muda yamphesa ya En-Gedi.