\c 1 \v 1 Nyimbo ya Nyimbo, yamene ni ya Solomoni.Mkazi azi kabisa yekha. \v 2 Ha, Mwakuti agani fiyofiyote ine naku fiyofiyotewa ndi pakamwa pake, \v 3 Mafuta yanu yozoza yokununkhira bwino; zina yako ndi mafuta onunkhira bwino, chifukwa chake atsikana amakukonda iwe. \v 4 Nditenge muyende naine ,Andipo tiza taba.