Sat Oct 02 2021 12:50:29 GMT+0200 (Central Africa Time)

This commit is contained in:
tsDesktop 2021-10-02 12:50:29 +02:00
parent 24ddb21098
commit fd4a6506bc
5 changed files with 9 additions and 1 deletions

1
02/23.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 23 Choncho ankakhala pafupi ndi antchito a Boazi kuti azikunkha mpaka kumapeto kwa nthawi yokolola balere ndi tirigu. Anakhala ndi apongozi ake.

1
03/01.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\c 3 \v 1 Naomi apongozi ake anati kwa iye, "Mwana wanga, kodi sindiyenera kukupezera malo oti upumulepo, kuti zinthu zikuyendere bwino? \v 2 Tsopano Boazi, munthu amene wakhala ukugwirira naye ntchito atsikanawa Kodi iye sadzakhala wachibale wathu? Taonani, akhala akupeta balere usikuuno popunthira.

1
03/03.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 3 Chifukwa chake, samba, nudzoze, ndi kuvala zovala zako zabwino kwambiri, nupita kumalo opunthira. Koma usadzidziwitse kwa mwamunayo kufikira atamaliza kudya ndi kumwa. \v 4 Koma akadzagona, ukaone pomwe wagona kuti upite kwa iye, ukamveketse mapazi ake, ugone pamenepo. \v 5 Ndipo Rute anati kwa Naomi, Ine ndidzacita zonse unenazi.

1
03/title.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
Mutu 3

View File

@ -58,6 +58,10 @@
"02-15",
"02-17",
"02-19",
"02-21"
"02-21",
"02-23",
"03-title",
"03-01",
"03-03"
]
}