Sat Oct 02 2021 12:56:31 GMT+0200 (Central Africa Time)

This commit is contained in:
tsDesktop 2021-10-02 12:56:31 +02:00
parent 2ab64199a0
commit efdc17b785
6 changed files with 11 additions and 2 deletions

View File

@ -1 +1 @@
\v 16 Rute atafika kwa apongozi ake, adati, "Mwakhala bwanji mwana wanga?" Kenako Rute anamuuza zonse zimene mwamunayo anamchitira. \v 17 Iye anati, "Miyezo isanu ndi umodziyi ya barele ndi yomwe wandipatsa, chifukwa anati, 'Musapite kwa apongozi anu opanda kanthu." \v 18 Zitheka, chifukwa munthuyo sadzapuma kufikira atamaliza chinthuchi lero. "
\v 16 Rute atafika kwa apongozi ake, adati, "Mwakhala bwanji mwana wanga?" Kenako Rute anamuuza zonse zimene mwamunayo anamchitira. \v 17 Iye anati, "Miyezo isanu ndi umodziyi ya barele ndi yomwe wandipatsa, chifukwa anati, 'Musapite kwa apongozi anu opanda kanthu." \v 18 Kenako Naomi anati, "Ukhale pano, mwana wanga, mpaka udziwe kuti zitheka bwanji, chifukwa munthuyo sadzapuma kufikira atamaliza ntchito imeneyi lero."

1
04/01.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\c 4 \v 1 Tsopano Boazi anakwera kuchipata ndipo anakhala pansi pomwepo. Posakhalitsa, wachibale wapafupi amene Boazi ananena za iye anadza. Bowazi anati kwa iye, "Bwenzi langa, bwera udzakhale pansi apa." Munthuyo anabwera nakhala pansi. \v 2 Kenako Boazi anatenga amuna khumi mwa akulu a mzindawo nati, "Khalani pansi apa." Kotero iwo anakhala pansi.

1
04/03.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 3 Bowazi anati kwa wachibale wapafupi uja, "Naomi, amene wabwera kuchokera kudziko la Mowabu, akugulitsa malo amene anali a Elimeleki mchimwene wathu. \v 4 Ndinaganiza zokukuwuza ndikuti, Ugule pamaso pa anthu amene ndakhala pano, pamaso pa akulu a anthu anga. ' Ngati ukufuna kuiwombola, uwombole. Koma ngati simukufuna kuiwombola, ndiuzeni kuti ndidziwe, chifukwa palibe wina amene angaiwombole kupatula iwe, ndipo ine ndiri pambuyo pako. ” Kenako munthu winayo anati, "Ndikuwombola."

1
04/05.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 5 Ndipo Boazi anati, "Tsiku lomwe udzagula mundawo kwa Naomi, utengere Rute Mmoabu, mkazi wamasiye wa munthu wakufa, kuti ukwezeke dzina la womwalirayo pa cholowa chake." \v 6 Kenako wachibale wapafupi uja anati, "Sindingathe kuziwombola ndekha popanda kuwononga cholowa changa. Utenge ufulu wanga wotiwombole wekha, chifukwa sindingathe kuuwombola."

1
04/title.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
Mutu 4

View File

@ -67,6 +67,11 @@
"03-08",
"03-10",
"03-12",
"03-14"
"03-14",
"03-16",
"04-title",
"04-01",
"04-03",
"04-05"
]
}