Sat Oct 02 2021 12:42:25 GMT+0200 (Central Africa Time)

This commit is contained in:
tsDesktop 2021-10-02 12:42:26 +02:00
parent e419778d9f
commit 03e7d58d5a
5 changed files with 9 additions and 1 deletions

1
01/22.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 22 Pamenepo Naomi ndi Rute, mkazi wachimowabu, mpongozi wake, anabwerera kuchokera kudziko la Mowabu. Adafika ku Betelehemu koyambirira kwa nthawi yokolola barele.

1
02/01.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\c 2 \v 1 Tsopano Naomi anali ndi m'bale wake wa mwamuna wake, mwamuna woyenera wa banja la Elimeleki, dzina lake Boazi. \v 2 Rute, mkazi wachimoabu adati kwa Naomi, "Ndiloleni ndipite ndikakunkhe zotsala pakati pa ngala za m'munda. Nditsata aliyense amene ndingakomere mtima wake." Natenepa Naomi ampanga, "Ndoko mwananga."

1
02/03.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
\v 3 Rute anapita kukakunkha zotsala m'minda atamaliza kukolola. Anafika ku minda ya Boazi, amene anali wa fuko la Elimeleki. \v 4 Ndipo onani, Boazi anachokera ku Betelehemu nati kwa okololawo, Yehova akhale nanu. Iwo anayankha kuti, "Yehova akudalitseni."

1
02/title.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
Mutu 2

View File

@ -45,6 +45,10 @@
"01-11",
"01-14",
"01-16",
"01-19"
"01-19",
"01-22",
"02-title",
"02-01",
"02-03"
]
}