Thu Mar 12 2020 15:28:52 GMT+0200 (South Africa Standard Time)

This commit is contained in:
Bshop2 2020-03-12 15:28:52 +02:00
parent 0c91b93edd
commit e7bc9df6d7
6 changed files with 11 additions and 6 deletions

View File

@ -1 +1 @@
\v 24 \v 25 Pamene nizapita ku Spain,nifuna kumuonani popitilapo,nakuti mukanitume imwe munjila yanga,pamene nizankhala na imwe panthawi itali.Koma apa niyenda ku Yerusalemu,kumikila okhulupilila.
\v 24 Pamene nizapita ku Spain, nifuna kumuonani popitilapo, nakuti mukanitume imwe munjila yanga, pamene nizankhala na imwe panthawi itali. \v 25 Koma apa niyenda ku Yerusalemu, kumikila okhulupilila.

View File

@ -1 +1 @@
\v 26 \v 27 Pakuti chinali ubwino wa Macedonia na Achia kupeleka ku osauka,pakati pa okhulupilila ali ku Yerusalemu.Inde chinali ku ubwino wao,nibankhongole bao,pakuti ngati akunja agabana muzauzimu zao,naiwonso afunika kuti abatumikile muzakuthupi.
\v 26 Pakuti chinali ubwino wa Macedonia na Achia kupeleka ku osauka, pakati pa okhulupilila ali ku Yerusalemu. \v 27 Inde chinali ku ubwino wao, nibankhongole bao, pakuti ngati akunja agabana muzauzimu zao, naiwonso afunika kuti abatumikile muzakuthupi.

View File

@ -1 +1 @@
\v 28 \v 29 Motelo ngati nasiliza ntchito iyi,nakusimikiza kuti balandila vamene vinatengewa,Nizayenda ku Spain nakumutandalilani munjila.Niziba kuti nikabwela kuli imwe nizabwela namadaliso mwa yesu ochuluka.
\v 28 Motelo ngati nasiliza ntchito iyi, nakusimikiza kuti balandila vamene vinatengewa, nizayenda ku Spain nakumutandalilani munjila. \v 29 Niziba kuti nikabwela kuli imwe nizabwela namadaliso mwa yesu ochuluka.

View File

@ -1 +1 @@
\v 30 \v 31 \v 32 Manje nimulimbikisani abale,mwa mbuye Yesu Christu,na chikondi cha muzimu,kuti muvutike naine mumapemphelo kwa Mulungu pali ine.Pemphelelani kuti nikapulumusiwe kulibaja osamnvela,mu ayaudeya nakuti utumiki wanga ukalandilidwe mu Yerusalemu ku okhulupilila,Pemphelani kuti nikabwele kuli imwe muchimwemwe,kupitila muchifunilo cha Mulungu,nakuti pamozi naimwe nikapeze kupumula/mupumulo.
\v 30 Manje nimulimbikisani abale,mwa mbuye Yesu Christu, na chikondi cha muzimu, kuti muvutike naine mumapemphelo kwa Mulungu pali ine. \v 31 Pemphelelani kuti nikapulumusiwe kulibaja osamnvela, mu ayaudeya nakuti utumiki wanga ukalandilidwe mu Yerusalemu ku okhulupilila, \v 32 Pemphelani kuti nikabwele kuli imwe muchimwemwe, kupitila muchifunilo cha Mulungu, nakuti pamozi naimwe nikapeze mupumulo.

View File

@ -1 +1 @@
\v 33 Mulungu wa mtendere ankhale naimwe monse.Amen.
\v 33 Mulungu wa mtendere ankhale naimwe monse. Amen.

View File

@ -235,6 +235,11 @@
"15-14",
"15-15",
"15-17",
"15-20"
"15-20",
"15-22",
"15-24",
"15-26",
"15-28",
"15-30"
]
}