Thu Mar 12 2020 13:44:13 GMT+0200 (South Africa Standard Time)

This commit is contained in:
Bshop2 2020-03-12 13:44:13 +02:00
parent cfec1fc96c
commit 35306be489
6 changed files with 10 additions and 5 deletions

View File

@ -1 +1 @@
\v 13 \v 14 Tiyeni tiyende moyenela,monga muzuba,osati mumaphwando yamuziko kapena muzolezelesa,ndipo tisayende muzadama,kapena zilakolako zosayenela,osati mukwiyo kapena nsanje,koma valani Yesu,ndipo musakhutise zakuthupi,kukwanilisa zilakolako zake.
\v 13 Tiyeni tiyende moyenela,monga muzuba, osati mumaphwando yamuziko kapena muzolezelesa, ndipo tisayende muzadama, kapena zilakolako zosayenela, osati mukwiyo kapena nsanje, \v 14 koma valani Yesu, ndipo musakhutise zakuthupi, kukwanilisa zilakolako zake.

View File

@ -1 +1 @@
\c 14 \v 1 \v 2 Landilani aliyense wofoka muchikhulupililo,osaweluza na mkangano.Munthu umozi alinachikhulupililo kudya chilichonse,wina wamene niwofoka akudya chabe zamasamba.
\c 14 \v 1 Landilani aliyense wofoka muchikhulupililo, osaweluza na mkangano. \v 2 Munthu umozi alinachikhulupililo kudya chilichonse, wina wamene niwofoka akudya chabe zamasamba.

View File

@ -1 +1 @@
\v 3 \v 4 Wamene akudya vilivonse asapepule wamene sakudya,ndipo wamene sakudya vonse asaweluze wamene akudya vonse.Pakuti Mulungu amulandila.Ndiwe ndani wamene uweluza kapolo wa munthu winangu?Anyamuka nakugwa pali mbuye wake.Koma azampanga kuimilila,pakuti ambuye akwanisa kupanga kuti aimilile.
\v 3 Wamene akudya vilivonse asapepule wamene sakudya, ndipo wamene sakudya vonse asaweluze wamene akudya vonse. Pakuti Mulungu amulandila. \v 4 Ndiwe ndani wamene uweluza kapolo wa munthu winangu? Anyamuka nakugwa pali mbuye wake. Koma azampanga kuimilila, pakuti ambuye akwanisa kupanga kuti aimilile.

View File

@ -1 +1 @@
\v 5 \v 6 Munthu umozi aona kuti siku imozi ipambana inanso.Wina aona masiku onse chimozi mozi.Lekani aliyense akhale nacho chisimikizo mumtima mwake.Wamene aona siku ayiyanganila kwa ambuye ndipo iye wakudya adyele mwa ambuye.chifukwa apeleka mayamiko kwa Mulungu.iye wamene sakudya,azichosako kudyela kwa Ambuye,naiyenso ayamika Mulungu.
\v 5 Munthu umozi aona kuti siku imozi ipambana inanso.Wina aona masiku onse chimozi mozi. Lekani aliyense akhale nacho chisimikizo mumtima mwake. \v 6 Wamene aona siku ayiyanganila kwa ambuye ndipo iye wakudya adyele mwa ambuye. Chifukwa apeleka mayamiko kwa Mulungu. Iye wamene sakudya,azichosako kudyela kwa Ambuye, naiyenso ayamika Mulungu.

1
14/title.txt Normal file
View File

@ -0,0 +1 @@
Mutu 14

View File

@ -210,6 +210,10 @@
"13-03",
"13-06",
"13-08",
"13-11"
"13-11",
"13-13",
"14-title",
"14-01",
"14-03"
]
}