nya-x-nyanja_rev_text_reg/13/12.txt

1 line
101 B
Plaintext

Nina ona chilombo china chichokela pa ziko yapansi. Chinali na nsengo zibili monga ka mwana ka nkhosa