\v 16 \v 17 Ndiponso bakulu bali 24 benze nkale pa mipando yao ya unfumu pamenso pa Mulungu bana zigwesa pansi pa nkope zao. Bana mu lambira Mulungu. Banati, "Tikuyamikani Ambuye Mulungu,