nya-x-nyanja_rev_text_reg/19/14.txt

1 line
374 B
Plaintext

\v 14 basilikali ba kumwamba banali kumulondola pa mahosi yoyera, ovala zovala zabwino, zoyera elo zopanda dothi. \v 15 mukamwa mwake muchoka mupeni wakutwa wamene amenyera maiko, azalamulira maiko na mphamvu. anaponda mothwela mpesa mu kukalipa kwa mulungu wa mphamvu. \v 16 ali na zina yolembewa pa chovala chake na pa chibelo chake: "mfumu ya mamfumu na mbuye wa ambuye."