nya-x-nyanja_rev_text_reg/09/10.txt

1 line
361 B
Plaintext

\v 10 Yanali na michila yolumila monga ya kaliza; ku michila yanali na mphamvu yoluma anthu kwa miyezi isanu. \v 11 Anali na wina monga mfumu pa iwo mngelo wa ku mugodi opanda kolekezera. Dzina lake mu chi heberi anali Abaddoni, ndipo mu chi greek anali na dzina lakuti Apollyon. \v 12 Soka loyamba lapita. Onani! pambuyo pa izi pali zilango zina zomwe zibwera.