nya-x-nyanja_rev_text_reg/09/07.txt

1 line
319 B
Plaintext

\v 7 Dzombe inaoneka monga kavalo okonzekera nkhondo. Pa mitu zao panali makolona agolide, ndipo nkhope zao zinali monga za munthu. \v 8 Anali na sisi monga mkazi, ndipo meno yanali monga ya nkhalamu. \v 9 Yanali na vobisa pa chifuwa monga va nsimbi, ndipo chongo chao chinali monga cha akavalo ambiri opita ku nkhondo.