nya-x-nyanja_rev_text_reg/04/01.txt

1 line
502 B
Plaintext

\c 4 \v 1 Pambuyo pa izi zinthu ninayang'ana, ndipo ninaona chiseko choseguka kumwamba. Mau oyamba omwe ninamva omwe yamakamba na ine monga lipenga kukamba ati, "bwera kuno, ndipo nizakuuza zamene zizachitika pambuyo pa izi." \v 2 Pa nthawi imeneyi ninali mu mzimu, ndipo ninaona kunali mpando wa chimfumu ku mwamba, ndipo panali wina onkhalapo. \v 3 Wamene analipo amaoneka monga jasper na carnelian. Panali utawaleza kuzungulira pa mpando wa mfumu. Utawaleza unaoneka umaoneka monga mwala wa emerald.