nya-x-nyanja_rev_text_reg/20/13.txt

1 line
336 B
Plaintext

\v 13 \v 14 \v 15 nyanja zinachosa bamene banaferamo. imfa na hadesi zinachosa bakufa bamene banalimo, elo bakufa banaweruziwa kulingana na zamene banachita. imfa na hadesi zinaponyewa mu nyanja ya muliro. uku nikufa kwa chiwiri- nyanja ya muliro. ngati zina ya wina aliyense sinalembewe mu buku la moyo, anaponyewa mu nyanja ya muliro.